STD 5 Chichewa Edited
STD 5 Chichewa Edited
STD 5 Chichewa Edited
MALANGIZO
1. Onetsetsani kuti pepala ili lili ndi masamba 5
2. Pepala ili lili ndi magawo anayi, Gawo: A, B. C ndi D.
3. Lembani dzina lanu ndi dzina la sukulu yanu pamwamba pa tsamba lino.
4. Lembani chimangirizo kapena kalata mugawo A, ndipo muyankhe mafunso onse mugawo B, C ndi D.
5. Yankhani mafunso a mugawo D pozunguliza lembo lokhoza lili lonse.
6. Perekani kwa wokuyang’anirani kulemba mayeso pepala lonseli nthawi yikakwana
GAWO A
Langizo Nanga tingasamale bwanji munthu
Yankhani funso limodzi mwa mafunso odwalayo
awiri ali m’munsiwa
Sankhani chimangirizo kapena kalata KAPENA
Mawu a chimangirizo chanu kapena 2. Lembani kalata kwa mzanu yemwe
kalata yanu asachepre 100 komanso akuphunzira kwina yomufotokozera za sukulu
asabzole 150 yanu. Mwa zina tsatani izi polemba